-
1 Mbiri 9:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pagulu la Alevi panali Semaya+ mwana wa Hasubu. Hasubu anali mwana wa Azirikamu ndipo Azirikamu anali mwana wa Hasabiya. Amenewa anali mbadwa za Merari.
-