Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezara 10:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho lolani kuti akalonga athu aimire anthu onse+ ndipo aliyense mʼmizinda yathu, amene wakwatira mkazi wachilendo, abwere pa nthawi imene ikhazikitsidwe. Abwere limodzi ndi akulu a mzinda uliwonse ndi oweruza ake, mpaka titabweza mkwiyo wa Mulungu wathu amene watikwiyira kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.”

      15 Koma Yonatani mwana wa Asaheli ndi Yahazeya mwana wa Tikiva anatsutsa zimenezi, ndipo Mesulamu ndi Sabetai,+ omwe anali Alevi, anawathandiza.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani