Deuteronomo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aisiraeli onse akabwera pamaso pa Yehova+ Mulungu wanu pamalo amene iye adzasankhe, muzidzawerenga Chilamulo ichi pamaso pa Aisiraeli onse kuti achimve.+ Nehemiya 8:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Machitidwe 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
11 Aisiraeli onse akabwera pamaso pa Yehova+ Mulungu wanu pamalo amene iye adzasankhe, muzidzawerenga Chilamulo ichi pamaso pa Aisiraeli onse kuti achimve.+