-
Yeremiya 17:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yehova wanena kuti: “Samalani kuti musanyamule katundu aliyense kapena kulowa naye pamageti a Yerusalemu pa tsiku la Sabata.+
-
-
Yeremiya 17:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Koma ngati simudzandimvera nʼkusiya kuona kuti tsiku la Sabata ndi lopatulika komanso mukadzanyamula katundu nʼkulowa naye pamageti a Yerusalemu pa tsiku la Sabata, ine ndidzawotcha ndi moto mageti a mzindawu. Motowo udzawotcha nsanja zokhala ndi mipanda yolimba za Yerusalemu+ ndipo sudzazimitsidwa.”’”+
-