-
Nehemiya 13:30, 31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Ndiyeno ndinawayeretsa ku zinthu zonse zodetsa za anthu a mitundu ina. Komanso ndinapereka ntchito kwa ansembe ndi Alevi, aliyense ndinamʼpatsa ntchito yake.+ 31 Ndinakonzanso zoti ena azibweretsa nkhuni+ pa nthawi zoikidwiratu ndiponso mbewu zoyamba kucha.
Inu Mulungu wanga, mundikumbukire pa zabwino zimene ndinachita.+
-