-
Deuteronomo 25:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azimukwapula pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikwapu zogwirizana ndi choipa chimene wachita.
-
-
Ezara 7:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Aliyense wosatsatira Chilamulo cha Mulungu wako ndi lamulo la mfumu, azipatsidwa chiweruzo msangamsanga, kaya choti aphedwe, athamangitsidwe, alipitsidwe kapena aikidwe mʼndende.”
-