-
Nehemiya 6:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani Tobia+ ndi Sanibalati komanso zimene anachitazi. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi ndi aneneri onse amene ankafuna kundiopseza.
-