-
Malaki 2:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Zikadzatero mudzadziwa kuti ine ndakupatsani lamulo limeneli kuti pangano limene ndinachita ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-