-
Ezara 2:43-54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Atumiki apakachisi:*+ Ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti, 44 ana a Kerosi, ana a Siyaha, ana a Padoni, 45 ana a Lebana, ana a Hagaba, ana a Akubu, 46 ana a Hagabu, ana a Salimai, ana a Hanani, 47 ana a Gideli, ana a Gahara, ana a Reyaya, 48 ana a Rezini, ana a Nekoda, ana a Gazamu, 49 ana a Uziza, ana a Paseya, ana a Besai, 50 ana a Asena, ana a Meyuni, ana a Nefusimu, 51 ana a Bakibuki, ana a Hakufa, ana a Harihuri, 52 ana a Baziluti, ana a Mehida, ana a Harisa, 53 ana a Barikosi, ana a Sisera, ana a Tema, 54 ana a Neziya ndi ana a Hatifa.
-
-
Ezara 8:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu oti akauze Ido ndi abale ake, atumiki apakachisi* omwe anali ku Kasifiyako kuti atibweretsere atumiki apanyumba ya Mulungu wathu.
-
-
Ezara 8:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kuchokera pa atumiki apakachisi* amene Davide ndi akalonga anawaika kuti azitumikira Alevi, panali atumiki a pakachisi 220. Onsewa anawasankha pochita kuwatchula mayina awo.
-