-
Yobu 15:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ine ndikuuza ndipo undimvetsere!
Ndikufotokozera zimene ndaona,
18 Zimene anthu anzeru amanena,
Zinthu zimene anamva kuchokera kwa makolo awo ndipo sanazibise.+
-