-
Yobu 1:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mwana wake aliyense wamwamuna ankakonza phwando kunyumba kwake pa tsiku limene wasankha.* Iwo ankaitana azichemwali awo atatu kuti adzadye ndi kumwera limodzi.
-