-
Yobu 30:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 “Tsopano anthu amene ndi aangʼono kwa ine,
Akundiseka.+
Anthu amene abambo awo sindikanalola
Kuwaika pamodzi ndi agalu olondera nkhosa zanga.
-