Yobu 9:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ngati iye akanasiya kundimenya,*Komanso kundiopseza ndi zinthu zake zochititsa mantha,+35 Ndikanalankhula naye mopanda mantha,Chifukwa ine sindiopa kulankhula.” Yobu 33:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
34 Ngati iye akanasiya kundimenya,*Komanso kundiopseza ndi zinthu zake zochititsa mantha,+35 Ndikanalankhula naye mopanda mantha,Chifukwa ine sindiopa kulankhula.”