-
Yobu 8:11-13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kodi gumbwa* angamere pamalo pamene si padambo?
Ndipo kodi bango lingakule popanda madzi?
12 Lidakali ndi maluwa, lisanadulidwe nʼkomwe,
Lidzauma zomera zonse zisanaume.
-