-
Salimo 69:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Bwerani pafupi ndi ine ndipo mundipulumutse.
Ndipulumutseni* kwa adani anga.
-
-
Salimo 103:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Moyo wanga utamande Yehova,
Ndisaiwale zinthu zonse zimene wachita.+
-