-
Yobu 4:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 ‘Kodi munthu angakhale wolungama kuposa Mulungu?
Kodi munthu angakhale woyera kuposa amene anamupanga?’
18 Iyetu sakhulupirira atumiki ake,
Ndipo angelo* ake amawapezera zifukwa.
-