-
Yobu 10:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiye nʼchifukwa chiyani munanditulutsa mʼmimba mwa mayi anga?+
Zikanakhala bwino ndikanafa diso lililonse lisanandione.
19 Zikanakhala ngati sindinakhaleko.
Ndikanangochokera mʼmimba nʼkupita kumanda.’
-
-
Yeremiya 15:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Tsoka ine, chifukwa inu mayi anga munabereka ine,+
Munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndi dziko lonse komanso kulimbana nalo.
Sindinakongole kanthu kapena kukongoza wina aliyense,
Koma anthu onse akunditemberera.
-