-
Yobu 41:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Palibe angalimbe mtima kuti aipute.
Ndiye ndi ndani amene angaimitsane ndi ine?+
-
-
Salimo 104:25, 26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Pali nyanja, yomwe ndi yakuya komanso yaikulu kwambiri,
Mmene muli zamoyo zosawerengeka, zazikulu ndi zazingʼono zomwe.+
-