-
Salimo 58:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Inu Mulungu, agululeni mano mʼkamwa mwawo.
Inu Yehova, thyolani nsagwada za mikango* imeneyi.
-
-
Miyambo 30:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pali mʼbadwo umene mano ake ndi malupanga
Ndiponso umene nsagwada zake ndi mipeni yophera nyama.
Mʼbadwowo umapondereza anthu ovutika apadziko lapansi
Komanso osauka pakati pa anthu.+
-