-
Salimo 72:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Adzakhala ngati mvula imene imagwera pa udzu umene watchetchedwa,
Ngati mvula yamvumbi imene imanyowetsa nthaka.+
-
-
Miyambo 16:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.
Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+
-