-
Yobu 1:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Iye anali ndi nkhosa 7,000, ngamila 3,000, ngʼombe 1,000 ndi abulu 500.* Analinso ndi antchito ambiri, moti anali munthu wolemekezeka kwambiri pa anthu onse a Kumʼmawa.
-