-
Mlaliki 7:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndi mapeto a munthu aliyense, ndipo amene ali ndi moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake.
-