-
Miyambo 28:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Aliyense amene amapereka zinthu zake kwa anthu osauka sadzasowa kanthu,+
Koma amene amatseka maso ake kuti asaone osaukawo adzalandira matemberero ambiri.
-