-
Yobu 10:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndimuuza Mulungu kuti: ‘Musanene kuti ndine wolakwa.
Ndiuzeni chifukwa chake mukulimbana nane.
3 Kodi mukupindula chilichonse mukamandizunza,
Mukamanyoza ntchito ya manja anu,+
Pamene mukugwirizana ndi zolinga za oipa?
-