-
Levitiko 19:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka kapena munthu wolemera.+ Ndipo muziweruza mwachilungamo.
-
-
Miyambo 24:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mawu awanso ndi a anthu anzeru:
Si bwino kukondera poweruza mlandu.+
-