-
Yobu 9:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Chifukwa iye wandivulaza ndi mavuto angati mphepo yamkuntho,
Ndipo wachulukitsa mabala anga popanda chifukwa.+
18 Sakulola kuti ndikokeko mpweya,
Ndipo akungopitiriza kuwonjezera mavuto anga.
-