Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+ Salimo 92:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+