-
Miyambo 5:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Chifukwa maso a Yehova amaona chilichonse chimene munthu akuchita,
Ndipo iye amafufuza njira zake zonse.+
-
-
Miyambo 15:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Maso a Yehova ali paliponse,
Amaona anthu oipa ndi abwino omwe.+
-
-
Yeremiya 16:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Chifukwa maso anga akuona chilichonse chimene akuchita.*
Anthuwo sanabisike kwa ine,
Ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.
-