1 Samueli 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndikumva chisoni kuti ndinaika Sauli kukhala mfumu. Iye wasiya kunditsatira, ndipo sanamvere mawu anga.”+ Samueli anakhumudwa kwambiri ndi nkhaniyi moti analirira Yehova usiku wonse.+
11 “Ndikumva chisoni kuti ndinaika Sauli kukhala mfumu. Iye wasiya kunditsatira, ndipo sanamvere mawu anga.”+ Samueli anakhumudwa kwambiri ndi nkhaniyi moti analirira Yehova usiku wonse.+