-
Salimo 68:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Imbirani iye amene wakwera pamwamba pa kumwamba,+ kumene kwakhalapo kuyambira kalekale.
Mawu ake amphamvu amamveka ngati bingu.
-