-
Yeremiya 31:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Yehova amene amapereka dzuwa kuti liziwala masana,
Amene amaika malamulo oti mwezi ndi nyenyezi ziziwala usiku,
Amene amavundula nyanja
Kuti mafunde ake achite phokoso,
Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti:+
-