Yeremiya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye ndi Mulungu amene anapanga dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zake,Amene anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru zake.+Amenenso anatambasula kumwamba chifukwa cha kuzindikira kwake.+
12 Iye ndi Mulungu amene anapanga dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zake,Amene anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru zake.+Amenenso anatambasula kumwamba chifukwa cha kuzindikira kwake.+