-
Yobu 7:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Nʼchifukwa chiyani simukundikhululukira machimo anga,
Nʼkunyalanyaza zolakwa zanga?
Chifukwa posachedwapa ndigona mʼfumbi,+
Ndipo mudzandifunafuna koma ine kudzakhala kulibe.”
-