Salimo 103:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+ Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+
17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+ Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+