-
Salimo 38:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Bwerani mwamsanga mudzandithandize,
Inu Yehova, amene mumandipulumutsa.+
-
-
Yesaya 12:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+
-