1 Samueli 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Doegi+ wa ku Edomu, mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti:+ “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu.+
9 Kenako Doegi+ wa ku Edomu, mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti:+ “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu.+