-
Salimo 94:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Inu Yehova, kodi anthu oipa adzapitiriza kusangalala mpaka liti?
Adzapitiriza kukondwera mpaka liti?+
4 Zolankhula zawo zimasonyeza kuti ndi opusa komanso onyada.
Anthu onse ochita zoipa amalankhula modzitama.
-