1 Samueli 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Doegi+ wa ku Edomu, mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti:+ “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu.+ 1 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, ipha ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi wa ku Edomu+ anapha ansembewo. Tsiku limenelo anapha amuna 85 ovala efodi wa nsalu.+ Salimo 109:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
9 Kenako Doegi+ wa ku Edomu, mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti:+ “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu.+
18 Ndiyeno mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, ipha ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi wa ku Edomu+ anapha ansembewo. Tsiku limenelo anapha amuna 85 ovala efodi wa nsalu.+