-
Yeremiya 18:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma inu Yehova,
Mukudziwa bwino ziwembu zawo zonse zimene andikonzera kuti andiphe.+
Musawakhululukire cholakwa chawo,
Ndipo musafafanize tchimo lawo pamaso panu.
-