-
Yesaya 40:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko,
Ndipo iye amawaona ngati fumbi limene lili pasikelo.+
Iyetu amanyamula zilumba ngati akunyamula fumbi.
-