-
Yobu 31:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ngati ndikudalira golide,
Kapena kuuza golide woyenga bwino kuti, ‘Ndimadalira iwe.’+
-
-
Yobu 31:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Chimenecho chikanakhala cholakwa chimene oweruza akuyenera kundipatsa chilango,
Chifukwa ndikanakhala nditakana Mulungu woona wakumwamba.
-