Yobu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ali ndi mtima wanzeru ndiponso mphamvu zambiri.+ Ndani angatsutsane naye koma osavulala?+ Nahumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+Koma Yehova salephera kulanga munthu woyenera kulangidwa.+ Njira yake ili mumphepo yowononga ndiponso yamkuntho.Ndipo mitambo ili ngati fumbi lopondapo mapazi ake.+ Chivumbulutso 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+Koma Yehova salephera kulanga munthu woyenera kulangidwa.+ Njira yake ili mumphepo yowononga ndiponso yamkuntho.Ndipo mitambo ili ngati fumbi lopondapo mapazi ake.+