- 
	                        
            
            Salimo 66:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        16 Bwerani mudzamve, inu nonse amene mumaopa Mulungu, Ndipo ine ndidzakuuzani zimene wandichitira.+ 17 Ndinamuitana ndi pakamwa panga, Ndipo ndinamutamanda ndi lilime langa. 
 
-