- 
	                        
            
            Salimo 5:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        11 Koma anthu onse amene amathawira kwa inu adzasangalala.+ Nthawi zonse adzafuula mosangalala. Inu mudzawateteza kuti anthu oipa asawafikire, Ndipo anthu okonda dzina lanu adzasangalala chifukwa cha inu. 
 
-