Salimo 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musakhale kutali ndi ine, chifukwa mavuto ali pafupi+Ndipo palibe winanso amene angandithandize.+ Salimo 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu Yehova, mwaona zimenezi. Choncho musakhale chete.+ Inu Yehova, musakhale kutali ndi ine.+ Salimo 38:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, musandisiye. Inu Mulungu, musakhale kutali ndi ine.+ 22 Bwerani mwamsanga mudzandithandize,Inu Yehova, amene mumandipulumutsa.+
21 Inu Yehova, musandisiye. Inu Mulungu, musakhale kutali ndi ine.+ 22 Bwerani mwamsanga mudzandithandize,Inu Yehova, amene mumandipulumutsa.+