Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • 1 Mbiri 22:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Tamvera, udzabereka mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wokonda mtendere ndipo ndidzachititsa kuti azikhala mwamtendere komanso asamavutitsidwe ndi adani ake omuzungulira.+ Nʼchifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo*+ ndipo mʼmasiku ake ndidzapatsa Aisiraeli bata ndi mtendere.+

  • Yesaya 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mulungu adzaweruza anthu a mitundu yosiyanasiyana

      Ndipo adzakonza zinthu zimene ndi zolakwika pakati pawo.

      Iwo adzasula malupanga awo kuti akhale makasu a pulawo,

      Ndipo mikondo yawo adzaisula kuti ikhale zida zosadzira mitengo.+

      Mtundu wa anthu sudzanyamula lupanga kuti umenyane ndi mtundu unzake,

      Ndipo anthuwo sadzaphunziranso nkhondo.+

  • Yesaya 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani