Salimo 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Munthu wopusa* amanena mumtima mwake kuti: “Kulibe Yehova.”+ Zochita zopanda chilungamo za anthu amenewa ndi zoipa komanso zonyansa,Ndipo palibe amene akuchita zabwino.+
53 Munthu wopusa* amanena mumtima mwake kuti: “Kulibe Yehova.”+ Zochita zopanda chilungamo za anthu amenewa ndi zoipa komanso zonyansa,Ndipo palibe amene akuchita zabwino.+