-
Salimo 94:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Inu Yehova, kodi anthu oipa adzapitiriza kusangalala mpaka liti?
Adzapitiriza kukondwera mpaka liti?+
-
-
Ezekieli 8:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi waona zimene akuluakulu a Isiraeli akuchita mumdima? Kodi waona zimene aliyense wa iwo akuchita mʼzipinda zake zamkati mmene muli mafano ake? Iwo akunena kuti, ‘Yehova sakutiona. Yehova wachokamo mʼdziko muno.’”+
-