-
Salimo 37:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ine ndaona munthu wankhanza komanso woipa
Zinthu zikumuyendera bwino ngati mtengo wa masamba obiriwira bwino panthaka yake.+
-