Salimo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipulumutseni ndi dzanja lanu, inu Yehova,Kwa anthu amʼdzikoli* amene gawo lawo lili mʼmoyo uno,+Anthu amene mwawakhutitsa ndi zinthu zabwino zimene mumapereka+Omwe amasiyira cholowa ana awo aamuna ochuluka.
14 Ndipulumutseni ndi dzanja lanu, inu Yehova,Kwa anthu amʼdzikoli* amene gawo lawo lili mʼmoyo uno,+Anthu amene mwawakhutitsa ndi zinthu zabwino zimene mumapereka+Omwe amasiyira cholowa ana awo aamuna ochuluka.